LyricFind Logo
LyricFind Logo
Profile image icon
Lyric cover art

Dobadosk1

Apple Music logo
Deezer logo
Spotify logo
Lyrics
Pachi dobadoba
Pachi dobadoski
Ndikuyenera kuti ndipange dollar
Ndikuyenera kuti ndipeze dollar yeah
Pachi dobadoba
Pachi dobadoski
Ndikuyenera kuti ndipange dollar
Ndikuyenera kuti ndipeze dollar uh

Amabwera ndi yolenga zi nkhani zawozawo zongopeka
Amaona ngati ngini ndiyophweka
Amabwera ndi ka Mpeni ku mphasa
Kuti andigwetse koma iwo akudabwa
Pachi dobadoski ndiku pusher P kuli kupewa ma loss
Iwe pachi doba-dolo kupanga ma Win kuti ndikhale boss

Pachi dobadoba
Pachi dobadoski
Ndikuyenera kuti ndipange dollar
Ndikuyenera kuti ndipeze dollar yeah
Pachi dobadoba
Pachi dobadoski
Ndikuyenera kuti ndipange dollar
Ndikuyenera kuti ndipeze dollar uh

Pachi dobadoba ndangovala nkanjo koma siine m'jomba uh
Singakhale sober
Bag yazaza ngati nduchoka kuma order
Undipeza chapa corner
Tili maso lero ndipo sitikugona
Ndikulanda dona, sindiopa olo utakhala Pona

WRITERS

Hasheem Msusa, Reuben Mtupanyama

PUBLISHERS

Lyrics © O/B/O DistroKid

Share icon and text

Share


See A Problem With Something?

Lyrics

Other

LyricIQ Analysis

Top Emotion

Enjoyment

Sentiment
Thumbsup Icon
Theme

Substance Use