Kuti ndidye n'mafunika hustle
N'mailowa dzuwa, pena ana ali pa kama
Dollar yake yobwera mojamamoja
Sin'ngaende mumdima n'kumezedwa ee
Mtulo mtima Ku window kuvetsera
Mkhutu mwadzadza mfuti, kulira mayi
Mzimu udachotsa udasala ndichani?
Wetter nthumba udachotsa udasala ndi mpeni
Chomwe walenga n'mabala ndi pain
Mseu omwe watengawo me sure you can return
When we try to get it tikuzingidwa
When we try to get it tikuzingidwa
Remember life is worth more than anything mmh
Sungagule ndi ndalama or anything no no
Nanga bwanji tingophana ngati zinyama
Dzuwa tinacheza naye lero wazama
Kulira Kwa ana ndimkazi, walira Nagama
Mwana anali yekhayo atani amama
See, the streets anuh safe now
Ukayenda wekha maso cheucheu
You can't trust your neba ndi moyo wakewo
Nanga popanda chifukwa mwayambitsa ndeu
When we try to get it tikuzingidwa
When we try to get it tikuzingidwa
When we try to get it tikuzingidwa
When we try to get it tikuzingidwa