Eyaaa ihh yeahh ih yeahhh
Aahhh pachiyambi tinali bho
Magaye amatisimba chi couple cha nyo
Mbiri yathu inali bho unali mkazi wa bho
Wa ulemu wodekha chi mami cha nyo
Koma lero umangondiyalusa
Pa line ndi ya ife moti tinatchuka
Umangobwebwetuka anthu kutiweluza
Mamveramvera ako ndi awa akutizunza
Daily kusintha amuna banja samalifuna
Kwawo ndikupasula lero ndi izo akuzembera wako iwe tachangamuka
Chonde nkhondo no pola moto eyaa
Nkhondo nkhondo no pola moto ummm
Po pola moto Pola motoooooo
Daily drama daily nkhondo
Kunyoza abale anga daily pokopoko
Kukhala nawe ndi chitonzo
Moti chikondi chonse chimapita
Ma plan amasintha lokakamiza limaswa mphika
Daily ma fever bp nkhani mpungwe mpungwe
Nsanje zozilengera nkhani zondipekela
Kaya ndiku-topa nane bola kungonena
Mtima umasweka kupilira kokha nde ndayesesa
Mwina ndi social media yi ikupusisa
Chonde pola moto nkhondo to to
Chonde nkhondo no pola moto eyaa
Nkhondo nkhondo no pola moto ummm
Po pola moto Pola motoooooo
Zachigulu pa nyumba anthu thot ho
Uzalira mayi ine Kalanga koto eyaiiii mmhhhh
Shode nkhondo no pola moto eyaaa
Nkhondo nkhondo no pola motoo mmmhhh
Po pola moto Pola motoooooo
Po pola moto Pola motoooooo